NSANJA YA OLONDA March 2014 | Kodi Ndi Zinthu Ziti Zimene Mulungu Wakuchitirani?

Mulungu anatipatsa moyo komanso amatipatsa zinthu zimene zimapangitsa kuti tizisangalala ndi moyo, koma kodi ndi zokhazi?

NKHANI YAPACHIKUTO

Kodi Ndi Zinthu Ziti Zimene Mulungu Wakuchitirani?

Mfundo yachilungamo yakuti “moyo kulipira moyo” ndi imene inapangitsa Mulungu kuti ‘apereke Mwana wake wobadwa yekha.’

NKHANI YAPACHIKUTO

Mwambo Womwe Simuyenera Kuuphonya

Tikukupemphani kuti mudzapezeke pa mwambo wokumbukira imfa ya Yesu.

MBIRI YA MOYO WANGA

Mavuto Anga Andithandiza Kulimbitsa Ubwenzi Wanga Ndi Yehova

Mzimayi amene amayendera njinga ya olumala anapeza “mphamvu yoposa yachibadwa” chifukwa cha chikhulupiriro chake.

Kodi Mulungu Amagwirizana Ndi Zoti Zipembedzo Zizichitira Zinthu Pamodzi?

Kodi anthu ayenera kulolera kuswa malamulo a m’Baibulo n’cholinga choti pakhale mtendere komanso mgwirizano? Mungadabwe ndi zimene Baibulo limanena pa nkhaniyi.

Mmene Mawu a Mulungu Anafikira ku Spain M’zaka za m’ma 500 Mpaka 1500 AD

Kodi ana a sukulu amene amalemba Malemba pamasileti akufanana bwanji ndi anthu amene ankalowetsa Mabaibulo mozemba m’dziko la Spain?

Kuyankha Mafunso a M’Baibulo

Kodi kuchimwa kwa munthu woyambirira, Adamu, kumagwirizana bwanji ndi imfa ya Yesu?

Zina zimene zili pawebusaiti

Kodi Baibulo Limati Chiyani pa Nkhani ya Isitala?

Werengani kuti mudziwe mmene miyambo 5 imene imachitika pa Isitala inayambira.