NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA) September 2015

M’magaziniyi muli nkhani zophunzira mlungu woyambira October 26 mpaka November 29, 2015.

Kodi Mukuyesetsa Kukhala Ngati Khristu?

Ngakhale kuti tatumikira Yehova kwa nthawi yaitali, tingalimbitsebe ubwenzi wathu ndi iye.

Kodi Chikumbumtima Chanu Chimakuthandizani Kusankha Zochita Mwanzeru?

Werengani kuti mudziwe zimene mungachite kuti chikumbumtima chanu chizikuthandizani kusankha bwino pa nkhani monga zaumoyo, zosangalatsa komanso kulalikira.

Khalani ndi Chikhulupiriro Cholimba

Kodi tikuphunzira chiyani pa zimene Petulo anachita poyenda pamadzi?

Kodi Yehova Amasonyeza Bwanji Kuti Amatikonda?

Kodi zimakuvutani kukhulupirira kuti Yehova amakukondani?

Kodi Tingasonyeze Bwanji Kuti Timakonda Yehova?

Tiyenera kuchita zambiri osati kungokonda Mulungu mumtima mwathu basi.

MBIRI YA MOYO WANGA

Madalitso a Yehova Andilemeretsa

Werengani mbiri ya moyo wa Melita Jaracz, amene anakhala mu utumiki wapadera kwa zaka zoposa 50 limodzi ndi mwamuna wake, Ted Jaracz, yemwe anali m’Bungwe Lolamulira.