NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA) January 2015

Magaziniyi ili ndi nkhani zophunzira kuyambira pa March 2, 2015 mpaka pa April 5, 2015.

Anadzipereka ndi Mtima Wonse ku New York

N’chiyani chinachititsa anthu okhala m’nyumba yabwino kwambiri kuti alolere kusamukira m’kanyumba kakang’ono kwambiri

Yamikani Yehova Ndipo Adzakudalitsani

Kodi mtima woyamikira ungatithandize bwanji pamene takumana ndi mavuto?

N’chifukwa Chiyani Timachita Mwambo Wokumbukira Imfa ya Yesu?

Kodi munthu angadziwe bwanji ngati adzapita kumwamba kapena adzakhala padzikoli?

Limbitsani Banja Lanu Kuti Likhale Losangalala

Pali zinthu 5 zimene zingathandize kuti banja likhale lolimba komanso losangalala.

Lolani Kuti Yehova Alimbitse Ndiponso Kuteteza Banja Lanu

Kodi mungatani kuti mupewe chigololo komanso mavuto amene amabwera ngati munthu atachita zimenezi?

Kodi N’zotheka Kukondana Mpaka Kalekale?

Kaya tikufuna kulowa m’banja kapena talowa kale, tikhoza kuphunzira zambiri m’Nyimbo ya Solomo.