NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA) December 2014

M’magaziniyi muli nkhani zophunzira kuyambira pa February 2 mpaka March 1, 2015.

‘Ankadziwa Njira Yake’

Guy H. Pierce, wa m’Bungwe Lolamulira la Mboni za Yehova, anamwalira Lachiwiri pa March 18, 2014.

Yehova Amadalitsa Anthu Opereka ndi Mtima Wonse

Kodi tikuphunzira chiyani pa zimene Aisiraeli anachita atapemphedwa ndi Mulungu kuti apereke zinthu zawo?

‘Mverani Ndipo Mumvetse Tanthauzo Lake’

Kodi mafanizo a Yesu onena za kanjere ka mpiru, zofufumitsa, wamalonda woyendayenda ndiponso chuma chobisika amatanthauza chiyani?

Kodi Timamvetsa Tanthauzo Lake?

Kodi mafanizo a Yesu onena za wofesa mbewu amene amagona, khoka ndiponso mwana wolowerera amatanthauza chiyani?

Kodi Mukukumbukira?

Mafunso 12 otsatirawa akuthandizani kukumbukira zimene mwaphunzira m’magazini a Nsanja ya Olonda kuyambira mu June mpaka mu December 2014.

Kodi Ndi Bwino Kusintha Maganizo Anu?

Kodi tingadziwe bwanji nthawi imene tiyenera kusintha maganizo ndi imene sitiyenera kusintha?

Mafunso Ochokera kwa Owerenga

Kodi Yeremiya ankatanthauza chiyani ponena kuti Rakele akulirira ana ake?

Tizigwirizana Kwambiri Pamene Mapeto Akuyandikira

Pali zitsanzo 4 za m’Baibulo zosonyeza ubwino wa kugwirizana. N’chifukwa chiyani nafenso tidzafunika kugwirizana kwambiri m’tsogolo?

Kodi Mumayamikira Zimene Muli Nazo?

Kodi tingasonyeze bwanji kuti timayamikira zimene taphunzitsidwa?

Mlozera Nkhani wa Magazini a Nsanja ya Olonda a 2014

Ndandanda wa nkhani zomwe zinatuluka mu 2014 m’magazini a Nsanja ya Olonda Yophunzira komanso Yogawira.