NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA) June 2014

M’magaziniyi muli nkhani zimene tidzaphunzire kuyambira August 4 mpaka 31, 2014.

“Salaza Njira ya Phazi Lako” Kuti Uyende Bwino

Kodi mungachotse bwanji chopinga chilichonse kuti mukwaniritse zolinga zanu?

Mafunso Ochokera kwa Owerenga

Kodi n’zoyenera kuti Akhristu azitentha mtembo?

Kodi Tingathandize Bwanji Akhristu Amene Banja Lawo Latha?

Onani mavuto amene amakhalapo ngati banja latha.

“Uzikonda Yehova Mulungu Wako”

Werengani nkhaniyi kuti mudziwe zimene Yesu ankatanthauza ponena kuti tizikonda Yehova ndi mtima wathu wonse, moyo wathu wonse ndiponso maganizo athu onse.

“Uzikonda Mnzako Mmene Umadzikondera Wekha”

Kodi Yesu ankatanthauza chiyani pamene ananena kuti tizikonda mnzathu? Nanga tingachite bwanji zimenezi?

Kodi Mukukumbukira?

Kodi mwawerenga mosamala magazini aposachedwapa a Nsanja ya Olonda? Tayesani kuyankha mafunso awa kuti muone zimene mukukumbukira.

Kodi Mumaona Anthu Ofooka Mmene Yehova Amawaonera?

Nkhaniyi itithandiza kuti tiziona moyenera abale ndi alongo amene amaoneka ngati ofooka.

Thandizani Ena Kuti Azichita Zonse Zimene Angathe

Kodi tingathandize bwanji abale achinyamata kapena atsopano kuti azichita zambiri mumpingo?