Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Mlozera Nkhani wa Magazini a Nsanja ya Olonda a 2007

Mlozera Nkhani wa Magazini a Nsanja ya Olonda a 2007

 Mlozera Nkhani wa Magazini a Nsanja ya Olonda a 2007

Wosonyeza deti la magazini imene muli nkhaniyo

BAIBULO

Baibulo Loyamba la Chipwitikizi, 7/1

Ernst Glück Anagwira Ntchito Yaikulu Zedi (kumasulira m’Chilativiya), 6/15

Inde, N’losavuta Kuwerenga, Koma Kodi N’lolondola? (Baibulo la Mphindi 100), 2/1

Kodi “Chipangano Chakale” Chinatha Ntchito? 9/1

Kodi Yesu Anali ndi Baibulo Lakelake, 12/1

Mabaibulo a Zinenero za mu Africa, 1/15

Malangizo Othandizadi, 4/1

Mapale Akale Amatsimikizira, 11/15

Mfundo Zazikulu za M’buku la Yesaya​—Gawo 2, 1/15

Mfundo Zazikulu za M’buku la Yeremiya, 3/15

Mfundo Zazikulu za M’buku la Maliro, 6/1

Mfundo Zazikulu za M’buku la Ezekieli, 7/1, 8/1

Mfundo Zazikulu za M’buku la Danieli, 9/1

Mfundo Zazikulu za M’buku la Hoseya, 9/15

Mfundo Zazikulu za M’mabuku a Yoweli ndi Amosi, 10/1

Mfundo Zazikulu za M’mabuku a Obadiya, Yona, ndi Mika, 11/1

Mfundo Zazikulu za M’mabuku a Nahumu, Habakuku, ndi Zefaniya, 11/15

Mfundo Zazikulu za M’mabuku a Hagai ndi Zekariya, 12/1

Mfundo Zazikulu za m’Buku la Malaki, 12/15

Mmene Mipukutu Inafikira Pokhala Baibulo Lathunthu, 6/1

“Mphatso Yamtengo Wapatali” ya Anthu a ku Poland, 8/15

Ntchito ya Alembi Akale, 3/15

MAFUNSO OCHOKERA KWA OWERENGA

Ana achikhristu akaphunzitsidwa bwino, ndiye kuti basi sadzasiya njira ya Yehova? (Miy. 22:6), 6/1

Kapolo wokhulupirika ndi “wanzeru”? (Mt 24:45), 9/1

Kodi Akhristu ayenera kupewa mankhwala a caffeine? 4/15

Kodi kusankha Akhristu odzozedwa kunatha liti? 5/1

“Mwamuna mmodzi mwa chikwi”? (Mlal. 7:28), 1/15

Kodi ndani ankakolola barele woyamba kucha? 7/15

Kodi njoka inali ndi miyendo? (Ge 3:14), 6/15

Kodi “nkhondo ya Haramagedo n’chiyani, (Chiv. 16:14, 16), 2/1

Kodi Nowa analowetsa nyama zingati zodyedwa m’chingalawa? 3/15

Kodi Yakobo analakwa kunamizira kuti anali Esau? (Ge 27:18, 19), 10/1

Kumenyanitsa matambula, 2/15

Kusindikiza chisindikizo (Chiv. 7:3), 1/1

“Mkazi wa mwamuna mmodzi,” (1Ti 5:9), 4/1

Mkhristu wa Mboni za Yehova akakhale nawo pamwambo wa ukwati wa anthu omwe si Mboni? 11/15

N’chifukwa chiyani Sauli anafunsa funso limeneli? (1Sa 17:58), 8/1

N’chifukwa chiyani Yesu anagwiritsa ntchito vinyo? 9/15

Nkhani ya Kusaka Kapena Kusodza? 12/1

MBIRI YA MOYO WANGA

Anatipulumutsa ku Ulamuliro Wankhanza (H. Dornik), 9/1

Chifukwa Chimene Ndimasangalalira Kupanga Ophunzira (P. Moseley), 2/1

Kutumikira Yehova Ndi Mwayi Waukulu Koposa (Z. Stigers), 8/1

Kuyenda Molowera ku Dziko Latsopano (J. Pramberg), 12/1

Munthu Amene Ankakonda Moyo Ndiponso Anthu (D. Sydlik), 1/1

Ndadalitsidwa Moyo Wanga Wonse Chifukwa Chosankha Bwino Zochita (P. Kushnir), 1/1

Ndakhala Ndikudikirira Ufumu Womwe “Suli Mbali ya Dziko Lino” (N. Gutsulyak), 3/1

Ndinaphunzira Kukhulupirira Yehova ndi Mtima Wonse (A. Baxter), 11/1

Ntchito Yopanga Ophunzira Yakhudza Kwambiri Zochita Pamoyo Wanga (L. Peters), 4/1

Tikukondwera Chifukwa ‘Anapambana Limodzi ndi Mwanawankhosa’ (C. Barber), 10/15

Tinafunitsitsa Kukwaniritsa Utumiki (L. Davison), 6/1

Tinapeza Chuma Chimene Tinkafufuza (D. Smith ndi D. Ward), 5/1

MBONI ZA YEHOVA

Chikhulupiriro cha Mayi Wina Chinapambana, 8/1

Chitsanzo cha Kuona Mtima, 2/15

“Chonde Landirani Kamphatso Kangaka” (Russia), 11/15

Mavuto Popereka Uthenga Wabwino (Africa), 10/15

Mayi wa Zaka Zoposa 100 Ali ndi Cholinga Pamoyo, 1/15

Mipata Youza Ena Chikhulupiriro Chanu? (anzanu kusukulu), 11/1

Misonkhano Yachigawo ya Chipulumutso Chayandikira (2006), 7/1

Mlandu Unatikomera ku Khoti Lalikulu ku Ulaya (Russia), 5/15

“Mphatso Yabwino Kwambiri” (Belgium), 12/15

“Mwayera Kale Ndipo M’mofunika Kukolola,” (Guajira Peninsula) 4/15

“Ndinamusirira Chifukwa Sanasinthe Maganizo Ake” (Germany), 10/15

“Nyumba ya Miyala” (Zimbabwe), 2/15

Omaliza Maphunziro a Gileadi, 1/1, 7/1

“Siliva Ndi Wanga, Golidi Ndi Wanga” (zopereka), 11/1

“Tsatirani Khristu!” Msonkhano Wachigawo, 3/1

Wolemala Koma Wodzipereka, 4/15

Zimene Adryana Analakalaka, 4/15

“Zozizwitsa” Ziwiri pa Msonkhano Umodzi (Georgia), 8/1

MOYO NDI MAKHALIDWE ACHIKHRISTU

Achinyamata Mumasangalatsa Mtima wa Makolo Anu, 5/1

“Anatiumiriza Kupita Basi!” 3/15

Kodi Mumangoganizira za Lero Zokha Basi? 10/15

Kodi Mumatsitsimula Ena? 11/15

Kodi Mungafutukule Chikondi Chanu? 1/1

Kodi Munthu Wauzimu Ndi Wotani? 8/1

Kodi Ndingatani Kuti Ndiphunzitse Bwino Ana Anga? 5/15

‘Kubala Zipatso Atakalamba,’ 9/15

Kukhulupirira Ulosi wa M’Baibulo, 4/1

Kunena Zoona? 2/1

Kupirira Zinthu Zopanda Chilungamo, 8/15

Kuwala N’kodabwitsa, 3/15

Lilime ndi Lamphamvu, 6/1

Londolani Kuwala, 10/15

Mdulidwe Umasonyeza Mwamuna Weniweni? 6/1

Mfundo Zodalirika Ndiponso Zosasinthasintha, 6/15

Moyo Wosangalala, 11/15

M’pofunika Kwambiri Kuyamikira Ena, 9/1

Mtima Wosamalira Ena, 6/15

Mungaphunzire Chiyani kwa Ana? 2/1

Musafooke Mwana Wanu Akapanduka, 1/15

Mwamuna ndi Mkazi Onse Ali ndi Udindo Wolemekezeka, 1/15

N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kusonkhana? 5/15

‘Ndiyeseni, Yehova,’ 8/15

Nsembe Zokondweretsa Mulungu, 4/1

“Nzeru Itchinjiriza” (Miy. 16), 7/15

Osangalala Kudikira Yehova, 3/1

Phunzitsani Ana Anu Kukonda Mtendere, 12/1

Phunzitsani Ana Anu Kukonda Mulungu, 9/15

Sitiyenera Kuchita Zinthu Monyanyira? 2/15

Si Zimene Munali Kuyembekezera, 4/15

Sonyezani ‘Chifundo Chachikulu,’ 12/15

‘Valani Kudzichepetsa,’ 11/1

“Zolingalira Zako Zidzakhazikika” (Miy. 16), 5/15

Zosankha Zimene Zimabweretsa Chisangalalo, 10/1

NKHANI ZOPHUNZIRA

Achinyamata​—Khalani ndi Zolinga Zolemekeza Mulungu, 5/1

Akazi, Muzilemekeza Kwambiri Amuna Anu, 2/15

Amuna, Muzitsanzira Umutu wa Khristu, 2/15

Ananu, Muzimvera Makolo Anu,” 2/15

‘Atate Wanu Ndi Wachifundo,’ 9/15

“Chenjerani ndi Kusirira kwa Nsanje kwa Mtundu Uliwonse,” 8/1

“Chirimikani, Ndipo Penyani Chipulumutso cha Yehova,” 12/15

“Iwe Uzikhala Wosangalala Basi” 1/1

Iwo Ndi Okalamba Koma Akubalabe Zipatso Zauzimu, 6/1

Khalani Okhulupirika kwa Khristu ndi kwa Kapolo Wake, 4/1

Kodi Inuyo Mumayembekezeradi Kuti Akufa Adzauka? 5/15

Kodi Muli ku Mbali ya Ulamuliro wa Yehova? 12/1

Kodi ‘Mupitiriza Kuyenda mwa Mzimu’? 7/15

Kodi Mwachimwira Mzimu Woyera? 7/15

Kodi Mwakonzekera Tsiku la Yehova? 12/15

Kodi Ndinu “Wolemera kwa Mulungu”? 8/1

Kodi Tingasonyeze Bwanji Chifundo? 9/15

Kodi Ziwanda Tingalimbane Nazo Bwanji? 3/15

Kuchita Chifuniro cha Mulungu Masiku Ano, 10/1

Kufufuza “Zinthu Zozama za Mulungu,” 11/1

Kufunafuna Cholinga Chabwino Pamoyo, 10/1

Kupirira Mavuto Kuli Ndi Ubwino Wake, 8/15

Kupulumutsidwa ku Misampha ya Wosaka Mbalame, 10/1

“Kuuka Koyamba” Kuli M’kati Panopa! 1/1

Lolani Mawu a Mulungu Kutsogolera Mapazi Anu, 5/1

Makhalidwe Okuthandizani Kupanga Ophunzira, 11/15

Makolo Phunzitsani Ana Anu Mwachikondi, 9/1

Mavuto Onse Adzatha Posachedwapa, 5/15

Mawu A Yehova Amakwaniritsidwa Nthawi Zonse, 11/1

Mpingo Uyenera Kulimbikitsidwa, 4/15

Mpingo Uyenera Kutamanda Yehova, 4/15

“Musabwezere Choipa pa Choipa,” 7/1

Musalekanitse Chimene Mulungu Anachimanga Pamodzi, 5/1

Musasiye Kukhala Oyamikira, 2/1

Mverani Chikumbumtima Chanu, 10/15

Okalamba Ndi Dalitso kwa Anthu Ocheperapo Msinkhu, 6/1

Opani Yehova Kuti Mukhale ndi Moyo Wosangalala, 3/1

Palibe Chida Chosulidwira Inu Chimene Chidzapambane, 12/15

Phunzitsani Ana Anu Kukonda Yehova, 9/1

Phunzitsani Zimene Baibulo Limaphunzitsa Kwenikweni, 1/15

Pirirani Poyembekezera Tsiku la Yehova, 7/15

“Pitirizani Kugonjetsa Choipa mwa Kuchita Chabwino,” 7/1

Thandizani Anthu Kumvera Zimene Baibulo Limaphunzitsa, 1/15

Tikweze Dzina la Yehova Pamodzi, 3/1

‘Tinapangidwa Modabwitsa,’ 6/15

Tizigonjera Abusa Achikondi Modzichepetsa, 4/1

Tsanzirani Wopanga Ophunzira Waluso, 11/15

Tsatirani Chikumbumtima Chanu, 10/15

Ulamuliro wa Yehova ndi Ufumu wa Mulungu, 12/1

Yehova Amakonda Chilungamo, 8/15

Yehova Amakondwera Mukamamumvera, 6/15

Yehova Ndi Mulungu Woyamikira, 2/1

NKHANI ZOSIYANASIYANA

“Anamanga Nyumba ya Isiraeli (Leya, Rakele), 10/1

Barizilai, 7/15

Bereya, 4/15

Buku la John Milton, 9/15

Chikhristu Chifalikira ku Asia Minor, 8/15

Chikondwerero cha Chikunja Chingakhale cha Chikhristu? 12/15

“Choonadi N’chiyani?” 10/1

Hana, 3/15

Jonatani Anachita Zinthu Mothandizidwa ndi Mulungu, 9/15

Kalendala Zaulimi ya mu “Dziko Lokoma,” 6/15

Kodi Muli ndi Mlangizi pa Zauzimu? 12/15

Kodi Mumaopa Zam’tsogolo? 5/15

Kodi Mzimu wa Munthu Sufa? 7/15

Kodi Nkhanza Zidzathadi? 4/15

Kodi N’zotheka Anthu Padziko Lonse Kugwirizana? 12/1

Kodi Tsankho Lingathe Bwanji? 7/1

Kodi Zoipa Zingathetsedwe? 6/1

Kulemba Kunali Kofunika Kwambiri ku Isiraeli, 8/15

Kulimbikitsa Makolo Oferedwa, 5/1

Luka Wantchito Mnzake Wokondedwa wa Paulo, 11/15

“Mboni Yokhulupirika Kuthambo,” 7/15

M’dziwe la Siloamu,” 7/15

Mungadziwe Kupembedza Koona? 3/1

Munthu Zikumuyendera Bwino? 1/1

Muyenera Kusamala Posankha Chipembedzo? 3/1

Samueli Analimbikitsa Kulambira Koona, 1/15

Sangalalani ndi Dziko Lapansi Lokongolali, 2/15

Saulo ndi Anzake Ndiponso Adani Ake, 6/15

Surakusa Mzinda Womwe Paulo Anaima Paulendo Wake, 10/15

Wessel Gansfort “Anali ndi Mfundo Zosintha Zinthu,” 3/1

“Ambuye, N’chifukwa Chiyani Simunachitepo Kanthu?” (Papa ku Auschwitz), 5/15

Amosi​—Wotchera Nkhuyu Kapena Wobaya Nkhuyu? 2/1

Yefita Anasunga Chowinda Chake kwa Yehova, 5/15

“Zombo za ku Kitimu” Panyanja, 10/15

YEHOVA

Dzina la Mulungu mu Nyimbo za ku Russia, 9/1

Kodi Chilengedwe N’chopandadi Mlengi? 8/15

Kodi Mulungu Amakuonani? 8/1

N’chifukwa Chiyani Mulungu Walola Kuti Zoipa Zizichitika? 9/15

YESU KRHISTU

Zinthu Zimene Khristu Adzachita Akabwera, 3/15