GALAMUKANI! November 2015 | N’chifukwa Chiyani Anthu Akusiya Zipembedzo Zawo?

Anthu ambiri akusiya kupita ku zipembedzo zawo. N’chifukwa chiyani anthuwa akuchita zimenezi?

NKHANI YAPACHIKUTO

N’chifukwa Chiyani Anthu Akusiya Zipembedzo Zawo?

Baibulo linaneneratu kuti anthu adzasiya kupita ku zipembedzo zawo.

Amachita Zinthu Bwinobwino Ngakhale Kuti Ndi Osaona

Munthu akasiya kuona, ubongo wake umasintha n’kuyamba kugwiritsa ntchito ziwalo zina. Anthu osaona amadalira kwambiri kumva mawu, fungo komanso amadalira manja ndi zala zawo kuti adziwe zinthu

KUCHEZA NDI ANTHU

Katswiri wa Masamu Akufotokoza za Chikhulupiriro Chake

N’chifukwa chiyani a Gene Hwang amaona kuti zimene Baibulo limanena sizitsutsana ndi kafukufuku amene anachita?

MFUNDO ZOTHANDIZA MABANJA

Muziyamikira Ana Anu

Kuyamikira mwana akachita khama n’kothandiza kwambiri.

ZIMENE BAIBULO LIMANENA

Kodi Dzikoli Lidzathadi?

Kodi mawu akuti “dziko,” omwe amapezeka pa 1 Yohane 2:17 amatanthauza chiyani? Kodi dziko limeneli lidzatha liti, nanga lidzatha bwanji?

KODI ZINANGOCHITIKA ZOKHA?

Zomera Nazonso Zimadziwa Masamu

Asayansi anachita kafukufuku pa zomera zinazake ndipo anapeza kuti zomerazi zimadziwa masamu kwambiri.

Zina zimene zili pawebusaiti

Mafunso Ofunsidwa Kawirikawiri

Pezani mayankho omveka bwino a mafunso amene anthu ambiri amakonda kufunsa.

Zoti Ana Achite

Gwiritsani ntchito zinthu zosangalatsa zimenezi, nkhani zochokera m’Baibulo komanso makadi a anthu otchulidwa m’Baibulo pophunzitsa ana mfundo za m’Baibulo.