GALAMUKANI! May 2014 | Kodi Mungatani Ngati Mukuvutika Maganizo?

Nthawi zina kuda nkhawa n’kwabwino kungoti zimatengera zimene mumachita mukamada nkhawa.

Zochitika Padzikoli

Nkhani zake ndi monga: dera limene kukumapezeka mitundu yoposa 100 ya nyama ndi zomera chaka chilichonse, maola oyenera kuti ana azionera TV ndi zimene anthu akuchita popanga magetsi osawononga zachilengedwe komanso zimene zikuwalepheretsa kuti akwaniritse cholingachi.

NKHANI YAPACHIKUTO

Kodi Mungatani Ngati Mukuvutika Maganizo?

Malangizo a m’Baibulo angakuthandizeni kuthana ndi kuvutika maganizo komwe nthawi zambiri kumayamba ndi zinthu 4.

MFUNDO ZOTHANDIZA MABANJA

Phunzitsani Ana Anu Kuti Azigwiritsa Ntchito Intaneti Moyenera

Kodi mungatani kuti musamangoikira mwana wanu malamulo koma muzimuphunzitsa kuti azitha kusankha zinthu mwanzeru?

KUCHEZA NDI ANTHU

Yemwe Anali Dokotala wa Opaleshoni Akufotokoza za Chikhulupiriro Chake

Kwa zaka zambiri, Dr. Guillermo Perez ankakhulupirira kuti zamoyo zinakhalako zokha, koma tsopano amakhulupirira kuti anthufe tinalengedwa ndi Mulungu. Kodi n’chiyani chinachititsa kuti ayambe kukhulupirira zimenezi?

Ntchito Yofufuza Anthu Amene Ankawaganizira kuti ndi Mfiti ku Ulaya

Zinthu zoopsa zimene zinachitika pa nthawi ina zinalimbikitsidwa ndi “buku loipa kwambiri . . . , komanso limene linachititsa kuti anthu ambiri azunzidwe.”

ZIMENE BAIBULO LIMANENA

Kusinkhasinkha

Sikuti kusinkhasinkha kulikonse n’kothandiza.

Nzeru Ikufuula—Kodi Inuyo Mukuimva?

Nzeru yeniyeni idzathetsa mavuto onse a anthu.

Zina zimene zili pawebusaiti

Kodi Ndine Munthu Wodalirika?

Achinyamata ena amapatsidwa ufulu wambiri poyerekezera ndi anzawo ena. Kodi n’chiyani chimachititsa kuti pakhale kusiyana kotereku?

Kodi Ndafika Poti N’kukhala ndi Chibwenzi?

Onani mafunso 4 amene angakuthandizeni kudziwa ngati mwafika poti n’kukhala ndi chibwenzi.

Kodi Makolo Anu Akufuna Kuthetsa Banja Lawo?

Kodi mungatani kuti musamangokhala wokhumudwa kapena wokwiya?

Zimene Achinyamata Amanena pa Nkhani ya Maonekedwe

N’chifukwa chiyani achinyamata ambiri zimawavuta kuti azisangalala ndi mmene amaonekera? N’chiyani chingawathandize pa nkhaniyi?

Mose Anakulira ku Iguputo

N’chifukwa chiyani amayi a Mose anabisa mwana wawoyu m’mbali mwa mtsinje wa Nailo? Werengani nkhaniyi kuti mudziwe zambiri zokhudza Mose, makolo ndi achibale ake, komanso mwana wamkazi wa Farao.