GALAMUKANI! May 2013 | Chenjerani ndi Mbava Komanso Anthu Ogwiririra

Anthu ambiri amaona kuti umbava, kugwiririra ndi zinthu zina za uchigawenga ndi vuto lalikulu kwambiri. Werengani nkhaniyi kuti mudziwe mmene mungadzitetezere.

Zochitika Padzikoli

Nkhani zake ndi monga: Apolisi alanda mfuti kumalo okwerera ndege, kusiyana kwa dziko la Norway ndi tchalitchi komanso njala ku India.

MFUNDO ZOTHANDIZA MABANJA

Zimene Mungachite Kuti Mwana Wanu Azikumverani

Cholinga cha chilango ndi kuphunzitsa. Mfundo za m’Baibulo zingakuthandizeni kuti muphunzitse mwana wanu kumvera.

NKHANI YAPACHIKUTO

Chenjerani ndi Mbava Komanso Anthu Ogwiririra

Kodi mungatani kuti muteteze moyo wanu komanso wabanja lanu?

KUCHEZA NDI ANTHU

Mzimayi Wachiyuda Anafufuzanso Mozama Zimene Ankakhulupirira

Kodi Racquel Hall anapeza umboni wotani womuthandiza kukhulupirira kuti Yesu anali Mesiya wolonjezedwa?

TIONE ZAKALE

Koresi Wamkulu

Kodi Koresi anali ndani, nanga ndi ulosi wochititsa chidwi uti wonena za iye umene unanenedwa kutatsala zaka 150 kuti iye abadwe?

ZIMENE BAIBULO LIMANENA

Mmene Mulungu Alili

Kodi Mulungu ndi munthu weniweni kapena ndi mphamvu chabe yosaoneka? Kodi Baibulo likamati anthu analengedwa m’chifaniziro cha Mulungu limatanthauza chiyani?

KODI ZINANGOCHITIKA ZOKHA?

Chigoba Chomwenso Chimaona

Werengani kuti mudziwe zambiri za kachilombo ka m’madzi kameneka.

Zina zimene zili pawebusaiti

Kodi Ndingatani Ngati Ndikudwala Matenda Aakulu?​—Gawo 1

Achinyamata 4 akufotokoza zimene zikuwathandiza kupirira matenda awo kuti asamangokhalira kudandaula.

Loti ndi Banja Lake—Zithunzi Zofotokoza Nkhani

Koperani nkhaniyi kuti mudziwe zimene mungaphunzire pa nkhani yokhudza banja la Loti.