NOVEMBER 19, 2018
ZATSOPANO
Baibulo la Dziko Latsopano Linatulutsidwa M’Chitetuni Dili
Pa 16 November, 2018, Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika linatulutsidwa m’chinenero cha Chitetuni Dili mumzinda wa Dili m’dziko la Timor-Leste. Baibulo la Dziko Latsopano lamasuliridwa lathunthu kapena mbali zake zina m’ziyankhulo 175.

