Pitani ku nkhani yake

ZATSOPANO

Baibulo Longomvetsera—Masalimo 73 Mpaka 89 Ayamba Kupezeka pa Intaneti

Baibulo Longomvetsera—Masalimo 73 Mpaka 89 Ayamba Kupezeka pa Intaneti

Panopa Buku Lachitatu la Masalimo (Masalimo 73 mpaka 89) longomvetsera lochokera mu Baibulo la Dziko Latsopano lachingelezi lokonzedwanso laikidwa pa jw.org.

Mvetserani Buku Lachitatu la Masalimo.