JUNE 22, 2020
RUSSIA
Palibe Chifukwa Choti Tiziopa Kuzunzidwa
Pamsonkhano wapachaka wa 2019, M’bale Mark Sanderson wa m’Bungwe Lolamulira anakamba nkhani yamutu wakuti, “Kodi Tiziopa Ndani?” Munkhaniyi munalinso vidiyo imeneyi yosonyeza abale ndi alongo athu ku Russia akufotokoza zimene zinawathandiza kuti asamaope kuzunzidwa.