NSANJA YA OLONDA September 2014 | Kodi Anthu Apitiriza Kuwononga Dzikoli N’kufika Poti Silingakonzedwenso?

Kodi anthu apitiriza kuwononga dzikoli n’kufika poti silingakonzedwenso?

NKHANI YAPACHIKUTO

Kodi Anthu Apitiriza Kuwononga Dzikoli N’kufika Poti Silingakonzedwenso?

Baibulo linaneneratu kuti anthu adzawononga chilengedwe, koma Mulungu sadzalola kuti aliwononge mpaka kufika poti silingakonzedwenso.

Kodi Malamulo Amene Mulungu Anapatsa Aisiraeli Anali Achilungamo?

Werengani nkhaniyi kuti mudziwe mfundo 4 zimene zinkathandiza oweruza a ku Isiraeli kuti aziweruza milandu mwachilungamo.

MBIRI YA MOYO WANGA

Kutumikira Mulungu Kwandithandiza Kuti Ndikhale Wosangalala

Zaka 65 zapitazo, Peter Carrbello anakumana ndi a Mboni za Yehova ndipo zimenezi zinapangitsa kuti moyo wake usinthe.

Baibulo Lotchedwa Peshitta Limatithandiza Kudziwa Zokhudza Mabaibulo Omwe Anamasuliridwa Kalekale

Baibulo lakale limeneli limasonyeza kuti Mabaibulo ena anaika mavesi amene sankapeza m’mipukutu yoyambirira.

Kuyankha Mafunso a M’Baibulo

Kodi tiyenera kupemphera kwa angelo kuti atithandize?

Zina zimene zili pawebusaiti

Kodi Ufumu wa Mulungu N’chiyani?

Dziwani chifukwa chake Ufumu wa Mulungu uli woposa boma lililonse la anthu.