NSANJA YA OLONDA

Tsamba 32

Chichewa
Tsamba 32
/assets/ct/79e1b14fff/images/syn_placeholder_sqr.png
Tsamba 32

Tsamba 32

▪ Kodi kusinkhasinkha za mmene nyenyezi zinapangidwira kungakuthandizeni motani? Onani tsamba 7.

▪ Kodi mungaphunzire chiyani ponena za Mulungu mukamaona mmene mayi amakondera mwana wake? Onani tsamba 9.

▪ N’chifukwa chiyani anthu okwatirana ayenera kumamvetserana wina akamalankhula ndiponso kuzindikira mmene wina akumvera? Onani tsamba 11.

▪ Kodi Ufumu wa Mulungu n’chiyani, nanga udzachita zotani padziko lapansili? Onani tsamba 16.

▪ Kodi ndi zinthu zina ziti zimene munthu amene akudwala matenda oti afa nawo amafunikira kwambiri? Onani tsamba 28.