NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA) April 2015

Magaziniyi ili ndi nkhani zophunzira kuyambira pa June 1 mpaka pa June 28, 2015.

Kodi Mumaphunzitsa Ena Kuti Akhalenso Akulu?

Onani mfundo 7 zimene akulu ena anena pa nkhani yophunzitsa ena.

Zimene Mungachite Pophunzitsa Ena Kuti Akhale Akulu

Akulu ayenera kuphunzitsa ngati Yesu ndipo ophunzira ayenera kutsanzira Elisa.

MBIRI YA MOYO WANGA

Ndadalitsidwa “M’nthawi Yabwino ndi M’nthawi Yovuta”

A Trophim Nsomba anapirira pamene ankazunzidwa. Mbiri ya moyo wawo ingakuthandizeni kuti mupitirizebe kukhala okhulupirika.

Kodi Yehova Ndi Mnzanu Weniweni?

Anthu akamalankhulana amagwirizana kwambiri. Ndi mmene zililinso ndi ubwenzi wathu ndi Yehova?

Muzikhulupirira Yehova Nthawi Zonse

Onani zimene zingakuthandizeni kulimbitsa ubwenzi wanu ndi Yehova.

Kuchotsa Anthu Osalapa Kumathandiza

Kodi kuchotsa anthu osalapa kumathandiza bwanji ngakhale kuti n’kopweteka?

Mtengo Ukadulidwa Umaphukanso?

Yankho la funsoli lingakuthandizeni kukhala ndi chiyembekezo.