NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA) March 2015

Magaziniyi ili ndi nkhani zophunzira kuyambira pa May 4 mpaka 31, 2015.

MBIRI YA MOYO WANGA

Tinapeza Ntchito Yofunika Kwambiri

David ndi Gwen Cartwright anali akatswiri ovina koma panopa amagwira limodzi ntchito yolalikira.

“Munavomereza Kuti Zimenezi Zichitike”

N’chifukwa chiyani gulu lasiya kufotokoza zinthu m’njira yosavuta?

Kodi ‘Mudzakhalabe Maso’?

Nkhaniyi ikusintha zinthu zina zimene tinkakhulupirira zokhudza fanizo la Yesu la anamwali 10. Ikungofotokoza mfundo yaikulu imene tikuphunzira pa fanizoli.

Mafunso Ochokera kwa Owerenga

N’chifukwa chiyani masiku ano mabuku anthu safotokoza kwambiri kuti zinthu zotchulidwa m’Baibulo zimaimira zinazake?

Kodi Tikuphunzira Chiyani pa Fanizo la Matalente?

Nkhaniyi ikusintha zinthu zina zimene tinkazikhulupirira pa fanizo la matalente.

Tizithandiza Abale a Khristu Mokhulupirika

Kodi nkhosa zimathandiza bwanji abale a Khristu?

Kodi N’zothekadi Kukwatira Kapena Kukwatiwa “Mwa Ambuye”?

Anthu amene amatsatira malangizo a Yehova amasangalala ndiponso kudalitsidwa.