MAGAZINI May 8, 2001 Ndende Zili Pamavuto Oopsa Kodi Njira Yothetsera Vutolo Ndiyo Ikulikulitsanso? Kodi Kusinthadi Ambanda N’kotheka? Dziko la Soviet Union Liukira Chipembedzo Amene Anaukiridwa Kwambiri ndi Soviet Union Mmene Zipembedzo Zinapulumukira Kodi Tsogolo la Chipembedzo N’lotani? Kusefukira kwa Madzi ku Mozambique—Momwe Akristu Anasamalira Anthu Ovutikawo Kodi Yehova Anali Mulungu wa Fuko la Ayuda? Kodi N’chifukwa Chiyani Ndiyenera Kudziŵana ndi Agogo Anga?