Lipoti la Chaka Chautumiki cha 2021 la Mboni za Yehova Padziko Lonse.

Onani mmene ntchito ya Mboni za Yehova yolalikira padziko lonse inayendera kuyambira mu September 2020 mpaka mu August 2021.

Ziwerengero Zonse za 2021

Lipoti la pa chakali likusonyeza khama komanso zinthu zomwe a Mboni za Yehova anawonongera pa ntchito yawo yolalikira yomwe ikuchitika padziko lonse.

Lipoti la Mayiko Komanso Madera la 2021

Lipotili likusonyeza ziwerengero za Amboni, anthu obatizidwa, opezeka pa Chikumbutso ndi zina.

Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi

MAFUNSO OFUNSIDWA KAWIRIKAWIRI

Kodi a Mboni za Yehova Alipo Angati Padziko Lonse?

Werengani kuti mudziwe mmene timapezera chiwerengero cha Mboni za Yehova.

MAFUNSO OFUNSIDWA KAWIRIKAWIRI

N’chifukwa Chiyani Mumalalikira Kunyumba ndi Nyumba?

Dziwani zimene Yesu anauza ophunzira ake oyambirira kuti azichita.

Mavidiyo Othandiza Muutumiki

Kodi a Mboni za Yehova ndi Anthu Otani?

Anthu ambiri amafuna atadziwa kuti a Mboni za Yehova ndi anthu otani. Onerani vidiyoyi kuti akuuzeni okha zimene amakhulupirira.

ZOKHUDZA IFEYO

Mboni za Yehova padziko lonse

Werengani kuti mudziwe mmene a Mboni za Yehova alili ogwirizana padziko lonse.

ZOKHUDZA IFEYO

Kodi Phunziro la Baibulo Limachitika Bwanji?

A Mboni za Yehova padziko lonse lapansi amadziwika bwino chifukwa cha ntchito yawo yophunzitsa anthu Baibulo kwaulere. Onani mmene amaphunzitsira.