Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

“Nyamulani Mwana Wanu”

“Nyamulani Mwana Wanu”

Mkazi wa ku Sunemu anachereza bwino kwambiri Elisa (2Mf 4:8-10)

Yehova anamudalitsa mayiyu ndipo anabereka mwana wamwamuna (2Mf 4:16, 17; w17.12 4 ¶7)

Yehova anagwiritsa ntchito Elisa kuti aukitse mwanayo (2Mf 4:32-37; w17.12 4 ¶8)

Kodi muli ndi chisoni chifukwa cha imfa ya mwana wanu? Yehova akumvetsa mmene mukumvera. Ndipo posachedwapa amuukitsa. (Yob 14:14, 15) Imeneyitu idzakhala nthawi yosangalatsa kwambiri.