Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Musamaiwale Kuti Muli mu Nthawi Yamapeto

Musamaiwale Kuti Muli mu Nthawi Yamapeto

Yehova anachenjeza Ayuda kuti adzawakana akapitiriza kuchita zoipa (2Mf 24:2, 3; w01 2/15 12 ¶2)

Yehova anagwiritsa ntchito Ababulo kuti awononge Yerusalemu mu 607 B.C.E. (2Mf 25:8-10; w07 3/15 11 ¶10)

Yehova anapulumutsa anthu amene anamvera machenjezo ake (2Mf 25:11)

Kwa zaka zambiri, Yehova wakhala akuchenjeza anthu padziko lapansi kuti adzawononga “anthu osaopa Mulungu.”​—2Pe 3:7.

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi ndimagwiritsa ntchito mpata uliwonse umene ndapeza kuti ndithandize ena kudziwa zimene Mulungu akutichenjeza?’​—2Ti 4:2.