Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Kodi Mapemphero Anga Amasonyeza Kuti Ndine Wotani?

Kodi Mapemphero Anga Amasonyeza Kuti Ndine Wotani?

Yabezi anali wolemekezeka kwambiri (1Mb 4:9)

Pemphero lake linasonyeza kuti ankaganizira kwambiri kulambira koona (1Mb 4:10a; w10 10/1 23 ¶3-7)

Yehova anayankha pemphero la Yabezi (1Mb 4:10b)

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi mapemphero anga amasonyeza kuti ndine wotani?’​—Mt 6:9, 10.