SEPTEMBER 24, 2018
ZATSOPANO
Baibulo la Dziko Latsopano Linatulutsidwa mu Chisena ndi Chitshwa
Baibulo la Dziko Latsopano Lomasulira Malemba Achigiriki Achikhristu linatulutsidwa mu Chisena ndi Chitshwa pa 21 September, 2018, mumzinda wa Maputo ku Mozambique. Baibulo la Dziko Latsopano lamasuliridwa lathunthu kapena mbali zake zina m’ziyankhulo 174.

