Zatsopano pa JW.ORG

2025-09-18

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)

Achikulire—Ndinu Ofunika Kwambiri Mumpingo

Achikulire ambiri amavutika ndi maganizo odziona kuti sangachite zambiri chifukwa cha mmene zinthu zilili pa moyo wawo panopa. Ndiye kodi angatani kuti alimbane ndi maganizo amenewa?

2025-09-18

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)

Kodi Mukukumbukira?​​—⁠December 2025

Kodi mwawerenga mosamala magazini a chaka chino a Nsanja ya Olonda? Taonani zimene mukukumbukira.

2025-09-18

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)

Mfundo Zothandiza Pophunzira​​—⁠Zimene Mungachite Kuti Muzikhulupirira Kwambiri Kuti Yehova Ali Ndi Mphamvu Zotha Kupulumutsa

Kodi mungatani kuti muzikhulupirira kwambiri Yehova?

2025-09-18

NYIMBO ZA BROADCASTING

Timakuona

Timanyadira alongo athu achikhristu kuzungulira dziko lonse lapansi.

2025-09-16

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)

December 2025

M’magaziniyi muli nkhani zophunzira kuyambira February 2–​March 1, 2026.

2025-09-15

NYIMBO ZA BROADCASTING

Muziwauza Kuti Mumawakonda

Onani mmene anthu omwe akukumana ndi zinthu zosiyanasiyana akusonyezera ena chikondi mwa mawu ndi zochita.

2025-09-08

NDANDANDA YA UTUMIKI KOMANSO MOYO WATHU WACHIKHRISTU

January–February 2026