Tanzania
Khoti Lalikulu Kwambiri ku Tanzania Lateteza Ufulu Wachibadwidwe wa Ana a Sukulu a Mboni
Oweruza onse a Khoti la Apilo ku Tanzania anapereka chigamulo chakuti sukulu za m’chigawo cha Mbeya zinaphwanya ufulu wolambira wa ana 127.