Sri Lanka
Msonkhano Wapadera Woyamba Kuchitikira ku Sri Lanka
A Mboni za Yehova masauzande ambiri ochokera m’mayiko 7 anakumana ndi abale ndi alongo awo auzimu ku Colombo pamsonkhano wapadera, ndipo umenewu unali woyamba kuchitikira ku Sri Lanka.
A Mboni za Yehova Anathandiza Anthu M’dziko la Sri Lanka Mutagwa Chimvula Choopsa
Patangodutsa zaka 12 kuchokera pamene ku Sri Lanka kunachitika tsunami, m’dzikoli munachitikanso ngozi ina ndipo a Mboni za Yehova anathandiza anthu omwe anakhudzidwa.