MALO A NKHANI

Germany

Chichewa
Germany
/assets/ct/28ada02fb0/images/syn_placeholder_sqr.png

Germany

 

2014-04-29

GERMANY

Bambo Richard Rudolph, Omwe Anapulumuka M’ndende Zozunzirako Anthu ku Germany, Amwalira Ali ndi Zaka 102

Bambo Richard Rudolph, omwe anali a Mboni za Yehova anamangidwa kwa zaka zoposa 19 chifukwa cha chikhulupiriro chawo.

2014-04-18

GERMANY

Mwambo Wokhazikitsa Chipilala Chokumbukira wa Mboni za Yehova Amene Anapulumuka Nkhanza ku Germany

Kodi n’chiyani chinathandiza Bambo Max Liebster, omwe anali a Mboni za Yehova, kupirira pamene ankazunzidwa kundende 5 zosiyanasiyana?

2013-11-25

GERMANY

Dziko la Germany Lapereka Mendulo Yaulemu kwa Mayi Wina wa Mboni za Yehova Poyamikira Ntchito Yake Yotamandika

Mathilde Hartl analandira mendulo yaulemu imene boma la Germany limapereka kwa anthu okhawo amene achita zinthu zazikulu. Anapereka menduloyi ndi nduna yaikulu ya chigawo cha Bavaria.