Malo a Nkhani
Lipoti la Bungwe Lolamulira la Nambala 6 la 2024
Mu lipotili, tiona zimene tingachite kuti tipitirize kuyambitsa maphunziro a Baibulo.
Lipoti la Bungwe Lolamulira la Nambala 5 la 2024
Mulipotili, tiona zimene tingachite kuti tizikhulupirira kwambiri kuti ndi Ufumu wa Mulungu wokha umene ungathetse mavuto onse amene anthufe tikukumana nawo.
Lipoti la Bungwe Lolamulira la Nambala 4 la 2024
Mu lipotili, tiona zimene abale ndi alongo athu amene ali m’ndende chifukwa cha zimene amakhulupirira akuchita kuti ‘apitirize kugonjetsa choipa pochita chabwino.’—Aroma 12:21.