Mboni za Yehova Padziko Lonse

Spain

  • Wa Mboni za Yehova akulalikira ku Spain

    Barcelona, Spain—A Mboni m’derali amalalikira m’zinenero monga Chiarabu, Chikatalani, Chingelezi, Chifulenchi, Chisipanishi komanso Chiudu

  • A Mboni za Yehova akulalikira ku Spain

    Ku Agaete pa zilumba za Canary m’dziko la Spain—Akugawira kabuku kakuti Uthenga Wabwino Wochokera kwa Mulungu!

Mfundo Zachidule—Spain

  • 48,693,000—Chiwerengero cha anthu
  • 125,359—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 1,369—Mipingo
  • Pa anthu 391 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

ZOCHITIKA PA MOYO

Nyumba Imene Munayesedwera Chikhulupiriro cha a Mboni Ena

Nyumba ya ku Spain yomwe inali ndende ya a Mboni za Yehova ambirimbiri omwe anakana kulowa usilikali chifukwa cha zimene amakhulupirira.

GALAMUKANI!

Dziko la Spain

Ku Spain kuli mitundu yambiri ya anthu komanso zinthu zachilengedwe zosiyanasiyana zochititsa chidwi. Ku Spain n’kumene kumapezeka mafuta a maolivi ambiri kuposa mayiko ena onse padziko lapansi.

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)

Masisitere Anasintha N’kukhala Alongo

N’chiyani chinawapangitsa kuchoka pamalo a masisitere kenako n’kusiya chipembedzo chawo chachikatolika?