Become Jehovah’s Friend—Posters

Posita: Yehova Akuthandiza Kuti Ukhale Wolimba Mtima

Panga dawunilodi n’kupulinta posita ya vidiyoyi imene ingakukumbutse kuti Yehova akuthandiza kuti ukhale wolimba mtima.

Posita: Uzisangalatsa Yehova

pangani dawunilodi ndi kusindikiza positayi kenako muiike pa zinthu zomwe munapanga dawunilodi.

Posita: Yehova Amakhululuka

Pangani dawunilodi ndi kusindikiza posita imene ikutiuza mmene Yehova amakhululukira anthu okhulupirika akalakwitsa zinazake.

Posita: Kodi Yehova Amayankha Mapemphero?

Pangani Dawunilodi n’kusindikiza posita ya vidiyoyi kenako muisunge pabwino.

Posita: Ndi Ndani Angakhale Mnzanga?

Sindikizani positayi ndi kuiika pamalo omwe muzitha kuiona pafupipafupi.