Pitani ku nkhani yake

Nkhani ya Yona Imatiphunzitsa Kukhala Olimba Mtima Komanso Achifundo

Yehova watuma mneneri Yona kuti akapereke uthenga wachiweruzo mumzinda wa Nineve m’dziko la Asuri koma iye akuchita zosemphana ndi zomwe wauzidwa. Mukamaonera vidiyoyi muona kuti Yona waphunzira kukhala wolimba mtima komanso wachifundo chifukwa cha zomwe wakumana nazo.

 

Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi

TSANZIRANI CHIKHULUPIRIRO CHAWO

Yona—Anaphunzira pa Zolakwa Zake

Kodi mungamvetse chifukwa chake Yona ankaopa kugwira ntchito imene Mulungu anamupatsa? Nkhani ya Yona ikutiphunzitse zambiri zokhudza kuleza mtima ndiponso chifundo cha Yehova.

TSANZIRANI CHIKHULUPIRIRO CHAWO

Yona—Anaphunzira Kufunika Kochitira Ena Chifundo

Kodi nkhani ya Yona ingatithandize bwanji kudzifufuza?