“Mulungu Anamuika Kukhala Ambuye Ndi Khristu”

Mkhristu akhoza kuyamba kukaikira ndipo chikhulupiriro chake chingayambe kufooka. Kuonera vidiyoyi kukuthandizani kuti muzikhulupira kwambiri Yesu, amene ndi Mesiya wolonjezedwa komanso Mfumu ya Ufumu wa Mulungu.

“Mulungu Anamuika Kukhala Ambuye Ndi Khristu” (Mbali Yoyamba)

N’chiyani chimakupangitsani kukhulupirira kuti Mulungu anamuika Yesu kukhala Ambuye ndi Khristu?

“Mulungu Anamuika Kukhala Ambuye Ndi Khristu” (Mbali Yachiwiri)

Onerani vidiyoyi kuti muzikhulupirira kwambiri Yesu.