‘Tiziyembekezera Zimene Sitikuziona’

Satana amafuna kuti tisakhale okhulupirika kwa Mulungu ndiponso kuti tisamakhale ndi chiyembekezo. Kodi tingatani kuti tikhalebe okhulupirika komanso kuona zinthu moyenera?

‘Tiziyembekezera Zimene Sitikuziona’—Mawu Oyamba

Banja lina likukumana ndi mavuto ofanana ndi amene anatchulidwa m’buku la Yobu. Ifenso tikhoza kukumana ndi mayesero ngati mmene zinakhalira ndi banjali. Komabe tikhoza kuthana nawo ndi thandizo la Yehova.

‘Tiziyembekezera Zimene Sitikuziona’

Vidiyo yokhudza mtimayi ingakuthandizeni kuti mukhalebe olimba mukakumana ndi mavuto ndiponso kuti muziyembekezerabe zimene Mulungu anatilonjeza.