Kodi Zinthu Zakumwamba ndi Padziko Lapansi Zinachita Kulengedwa?

Kodi Zinthu Zakumwamba ndi Padziko Lapansi Zinachita Kulengedwa?

M’chilengedwechi muli zinthu zambiri ndiponso zochititsa chidwi. Kodi zinthu zonsezi zinakhalapo bwanji? Kodi zimene Baibulo limanena zokhudza mmene chilengedwe chinayambira ndi zomveka?