Pulogalamu ya Msonkhano Wadera Wokhala ndi Woyang’anira Dera wa 2026-2027
“Wosangalala ndi Munthu Amene Amadalira Yehova”
Pulogalamu yosonyeza chigawo cha m’mawa ndi masana cha msonkhano wadera wokhala ndi woyang’anira dera.
Mupeze Mayankho a Mafunso Awa
Mafunsowa adzayankhidwa pamsonkhanowu.

