Pulogalamu ya Msonkhano Wadera Wokhala ndi Woimira Nthambi wa 2026-2027
‘Muzisangalala Chifukwa cha Yehova’
Pulogalamu ya chigawo cha m’mawa ndi masana ya msonkhano wadera wokhala ndi woimira nthambi.
Mupeze Mayankho a Mafunso Awa
Mafunsowa adzayankhidwa pamsonkhanowu.

