Pulogalamu ya Msonkhano Wadera Wokhala ndi Woyang’anira Dera wa 2025-2026
‘Muzilambira Motsogoleredwa Ndi Mzimu Ndi Choonadi’
Pulogalamu yosonyeza chigawo cha m’mawa ndi masana cha msonkhano wadera wokhala ndi woyang’anira dera.
Mupeze Mayankho a Mafunso Awa
Mafunsowa adzayankhidwa pamsonkhanowu.

