Pulogalamu ya Msonkhano wa 2023 wakuti “Khalani Oleza Mtima”

Lachisanu

Pulogalamu ya Lachisanu yachokera palemba la 1 Akorinto 13:4​—“Chikondi n’choleza mtima.”

Loweruka

Pulogalamu ya Loweruka ikuchokera palemba la 1  Atesalonika 5:14​—“Khalani oleza mtima kwa onse.”

Lamlungu

Pulogalamu ya Lamlungu yachokera pa lemba la Yesaya 30:18​—‘Yehova akuyembekezera moleza mtima kuti akukomereni mtima.’

Mawu kwa Osonkhana

Mfundo zothandiza kwa omwe asonkhana.

Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi

ZOKHUDZA IFEYO

Dzabwereni ku Msonkhano wa 2026​​—⁠“Chimwemwe Chosatha”

Tikukuitanirani ku Msonkhano wa masiku atatu wachaka chino wa Mboni za Yehova.

MISONKHANO IKULUIKULU

Tikukuitanani ku Msonkhano wa Mboni za Yehova wa 2023 Wakuti, “Khalani Oleza Mtima”

Tikukulandirani ndi manja awiri kumsonkhano wa masiku atatu wa Mboni za Yehova wa chaka chino.

MISONKHANO IKULUIKULU

Zimene Zili Muvidiyo Yakuti: ’Muzilola Kuti Yehova Akutsogolereni’

Onani mmene tingaphunzire kudalira kwambiri Yehova pamene takumana ndi mavuto.