NSANJA YA OLONDA August 2015 | Kodi Anthu Amene Anamwalira Adzakhalanso Ndi Moyo?

Baibulo limayankha funso limeneli ndiponso limapereka umboni wotsimikizira kuti zimenezi zidzachitikadi.

NKHANI YAPACHIKUTO

Kodi Chimachitika N’chiyani Munthu Akamwalira?

Baibulo limafotokoza zokhudza anthu 8 amene anaukitsidwa. Kodi anthuwa anafokoza chilichonse chokhudza zomwe zinkachita atamwalira?

NKHANI YAPACHIKUTO

Kodi Akufa Angadzakhalenso ndi Moyo?

N’chifukwa chiyani Mulungu adzaukitse anthu osalungama?

NKHANI YAPACHIKUTO

Tingatsimikize Bwanji Kuti Amene Anamwalira Adzakhalanso Ndi Moyo?

Baibulo limapereka zifukwa ziwiri zokhulupirira kuti akufa adzakhalanso ndi moyo.

MBIRI YA MOYO WANGA

Yehova Wandichitira Zazikulu

Félix Alarcón anaona kuti moyo wake uli ndi tsogolo labwino pambuyo pa ngozi ya njinga yamoto yomwe inapangitsa kuti afe ziwalo kuchokera khosi kupita m’munsi.

TSANZIRANI CHIKHULUPIRIRO CHAWO

“Ine Ndinauka Monga Mayi mu Isiraeli”

Kodi tingaphunzire chiyani zokhudza kulimba mtima komanso chikhulupiriro pa nkhani ya m’Baibulo yonena za Debora

Kuyankha Mafunso a M’Baibulo

Kodi tinalengedwa kuti tizingokhalako kwa nthawi yochepa? Kodi Mulungu anatilengeranji?

Zina zimene zili pawebusaiti

Kodi Mungatani Kuti Musamaope Kwambiri Imfa?

Kusaopa kwambiri imfa kungakuthandizeni kuti muzisangalala ndi moyo.