NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA) March 2025

M’magaziniyi muli nkhani zophunzira kuyambira May 5–June 8, 2025.

NKHANI YOPHUNZIRA 9

Musachedwe Kubatizidwa

Idzaphunziridwa mlungu woyambira May 5-11, 2025.

NKHANI YOPHUNZIRA 10

Tizitsanzira Mmene Yehova ndi Yesu Amaganizira

Idzaphunziridwa mlungu woyambira May 12-18, 2025.

NKHANI YOPHUNZIRA 11

Muzilalikira Mwakhama Ngati Yesu

Idzaphunziridwa mlungu woyambira May 19-25, 2025.

NKHANI YOPHUNZIRA 12

Pitirizani Kuyenda Motsogoleredwa ndi Chikhulupiriro

Idzaphunziridwa mlungu woyambira May 26–June 1, 2025.

NKHANI YOPHUNZIRA 13

Dzanja la Yehova Si Lalifupi

Idzaphunziridwa mlungu woyambira June 2-8, 2025.

MFUNDO ZOTHANDIZA POPHUNZIRA

Muzigwiritsa Ntchito Baibulo Ngati Galasi

Kodi mungagwiritse ntchito bwanji Baibulo ngati galasi?