NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA) May 2019

M’magaziniyi muli nkhani zophunzira kuyambira July 1 mpaka August 4, 2019.

Tizisonyeza Chikondi ndi Chilungamo Mumpingo

Kodi chilamulo cha Khristu n’chiyani, nanga chimalimbikitsa bwanji chilungamo?

Tizisonyeza Chikondi ndi Chilungamo M’dziko Loipali

Kodi makolo angateteze bwanji ana awo kuti asagwiriridwe, nanga akulu angateteze bwanji mpingo?

Tizilimbikitsa Anthu Amene Achitiridwa Zoipa

Kodi anthu amene anagwiriridwa angalimbikitsidwe bwanji ndi Mawu a Mulungu, akulu komanso Akhristu olimba mwauzimu?

Tisapusitsidwe ndi “Nzeru za M’dzikoli”

N’chifukwa chiyani Yehova ali woyenera kutipatsa malangizo? Kodi Baibulo limatithandiza bwanji kuti tizidziona moyenera?

Muziyesetsa Kuti Kuphunzira Kuzikuthandizani!

Kodi tingatani kuti tizikhala ndi nthawi yophunzira komanso kuti tizipindula kwambiri tikamaphunzira Baibulo?