GALAMUKANI! June 2015 | Mfundo 5 Zomwe Zingakuthandizeni Kuti Mukhale ndi Moyo Wathanzi
Zimene mumachita pa nkhani ya ukhondo zingachititse kuti musamadwaledwale komanso kuti mupeweretu matenda ena.
NKHANI YAPACHIKUTO
Zimene Mungachite Kuti Mukhale Ndi Moyo Wathanzi
Werengani mfundo 5 zomwe zingakuthandizeni kuti mukhale ndi moyo wathanzi.
MFUNDO ZOTHANDIZA MABANJA
Mungatani Kuti Mukwaniritse Lonjezo Lanu?
Kodi mumaona kuti lonjezo laukwati lili ngati goli loti simungathe kuchokamonso kapena mumaona kuti lili ngati nangula?
TIONE ZAKALE
Galileo
Mu 1992, Papa Yohane Paulo Wachiwiri anavomereza kuti tchalitchi cha Katolika chinalakwitsa kuimba Galileo mlandu chifukwa cha ntchito yake.
Nsomba Zomwe Zimapanga Mchenga
Nsombazi zimathandiza kwambiri kuti zomera zam’madzi zizikula bwino komanso kuti m’madzi mukhale mwaukhondo.
ZOCHITIKA PADZIKOLI
Nkhani Zokhudza Chilengedwe
Nkhani zaposachedwapa zikupangitsa kuti anthu azidzifunsa kuti, “N’chifukwa chiyani anthu akulephera kuthetsa vuto la kuwononga chilengedwe?”

