GALAMUKANI! December 2014 | Zimene Muyenera Kudziwa Zokhudza Matenda a Muubongo
Matenda a muubongo ndi oopsa kwambiri koma anthu ambiri amene ali ndi vutoli sapita kuchipatala kuti akalandire thandizo. Chifukwa chiyani?
NKHANI YAPACHIKUTO
Zimene Muyenera Kudziwa Zokhudza Matenda a Muubongo
Zinthu 9 zomwe zingakuthandizeni ngati mukudwala matenda a muubongo.
Zochitika Padzikoli
Nkhani zake: nyama yomwe yakhala ndi moyo nthawi yaitali kuposa zonse, nyanja yomwe yatsala pang’ono kuuma ndi nthawi yomwe anthu ambiri amadwala matenda a mtima.
MFUNDO ZOTHANDIZA MABANJA
Kodi Mungatani Kuti Muzilolerana M’banja?
Mfundo 4 zomwe zingakuthandizeni kuti musamangokangana koma muzipeza njira zothetsera mavuto.
Kanyama Kakang’ono ka Maso Aakulu
Diso lililonse la kanyamaka ndi lalikulu kuposa ubongo wake.
KUCHEZA NDI ANTHU
Katswiri wa Zachuma Akufotokoza za Chikhulupiriro Chake
Pulofesa Stephen Taylor ananena kuti kuphunzira Baibulo kunali ngati kusunga chuma choti chidzamuthandize m’tsogolo.
Mlozera Nkhani wa Magazini a Galamukani! a 2014
Nkhani zomwe zinatuluka m’magazini a Galamukani! a 2014.

