GALAMUKANI! March 2008 Kodi Pali Chipembedzo Choona Chimodzi Chokha? Ndani Angatisonyeze Chipembedzo Choona? Kodi Mungapeze Bwanji Chipembedzo Choona? Kodi Zikhulupiriro za Makolo N’zogwirizana ndi Baibulo? Kulalikira Uthenga Wabwino ku Madera Akutali N’chifukwa Chiyani Chimatchedwa Chilumba Chachikulu? Anyani Odabwitsa a M’matanthwe Kodi Kutukwana N’kulakwadi? Miyambo Yakale Ilipobe ku Mexico Akasupe a Madzi Otentha Diso la Njuchi Zochitika Padzikoli “Tsiku Limene Kunada Masana” Kuchokera kwa Owerenga Kodi Mungayankhe Bwanji?