MAGAZINI October 8, 2000 Thambo Lathu Lodabwitsali—Kodi Linangokhalako Mwamwayi? Kodi Maelementi Anakhalako Mwamwayi? Dziko Lapansi—Kodi “Maziko” Ake Anakhalako Mwamwayi? N’chifukwa Chiyani Ndili Wochepa Thupi Chonchi? Nyamalikiti—Nyama Zamisinkhu Yaitali, Zamiyendo Yaitali, Ndiponso Zokongola Kukhalabe Okhulupirika mu Ulamuliro Wankhanza Kodi “Ntchito Yokhazikika” Idamka Kuti? “Maseŵera Angozi”—Kodi Muyenera Kuika Moyo Wanu Pachiswe Mwakuwachita? Chimene Ndimaikirapo Mtima Kwambiri Ndicho Kukhalabe Wokhulupirika