CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

‘Kodi Munthu Angakhale Waphindu kwa Mulungu?’

‘Kodi Munthu Angakhale Waphindu kwa Mulungu?’

Elifazi ananena kuti Mulungu amaona kuti ndife opanda phindu (Yob 22:​1, 2; w05 9/15 27 ¶1-3)

Elifazi ananenanso kuti Mulungu alibe nazo ntchito zoti ndife olungama kapena ayi (Yob 22:3; w95 2/15 27 ¶6)

Zochita zathu zingachititse kuti Yehova ayankhe Satana yemwe amamutonza (Miy 27:11; w03 4/15 14-15 ¶10-12)

FUNSO LOFUNIKA KULIGANIZIRA: Kodi mumamva bwanji mukaganizira kuti Wamphamvuyonse amakuonani kuti ndinu wofunika?