NDANDANDA YA UTUMIKI KOMANSO MOYO WATHU WACHIKHRISTU July–August 2023 ONANI ZONSE MITU YAIKULU July 3-9 Onani Zowonjezera “Musakalowerere Ntchito Yomanga” “Kuteteza . . . ndi Kukhazikitsa Mwalamulo Ntchito ya Uthenga Wabwino” July 10-16 Onani Zowonjezera Zochita za Ezara Zinachititsa Kuti Dzina la Yehova Lilemekezedwe July 17-23 Onani Zowonjezera Kusamvera Kumapweteketsa July 24-30 Onani Zowonjezera “Nthawi Yomweyo Ndinapemphera” July 31–August 6 Onani Zowonjezera Kodi Mumagwira Ntchito Zonyozeka? August 7-13 Onani Zowonjezera Nehemiya Ankafuna Kutumikira, Osati Kutumikiridwa Amachita Khama Kuti Atitumikire August 14-20 Onani Zowonjezera “Chimwemwe Chimene Yehova Amapereka Ndicho Malo Anu Achitetezo” Zochita Zanu Zingathandize Banja Lanu Kukhala Losangalala August 21-27 Onani Zowonjezera Anasiya Zinthu Zina Chifukwa cha Yehova Kodi Muli ndi Zolinga Zotani M’chaka Chautumiki Chikubwerachi? Ntchito Yapadera Yolengeza za Ufumu wa Mulungu mu September August 28–September 3 Onani Zowonjezera Muzikhala Okhulupirika kwa Yehova Mukamasankha Anthu Ocheza Nawo Tsanzirani Chikondi Chokhulupirika cha Yehova Zimene Tinganene