PULOGALAMU YA MSONKHANO WADERA WOKHALA NDI WOIMIRA NTHAMBI WA 2025-2026

Mupeze Mayankho a Mafunso Awa

Chichewa
Mupeze Mayankho a Mafunso Awa
/assets/ct/28ada02fb0/images/syn_placeholder_sqr.png
CA-brpgm26 tsamba 4

Mupeze Mayankho a Mafunso Awa

Mupeze Mayankho a Mafunso Awa
  1. 1. Kodi tingamve bwanji “zimene mzimu ukunena”? (Chiv. 1:3, 10, 11; 3:19)

  2. 2. Kodi n’chiyani chingatithandize kuti tipitirizebe kuchita khama komanso kupirira? (Chiv. 2:4)

  3. 3. Kodi tingakonzekere bwanji kuti tidzathe kupirira molimba mtima tikamadzazunzidwa? (Miy. 29:25; Chiv. 2:10, 11)

  4. 4. Kodi tingatani kuti tisakane kuti timakhulupirira Yesu? (Chiv. 2:12-16)

  5. 5. Kodi tingatani kuti tipitirize kugwira mwamphamvu chimene tili nacho? (Chiv. 2:24, 25; 3:1-3, 7, 8, 10, 11)

  6. 6. Kodi n’chiyani chingatithandize kukhalabe odzipereka? (Chiv. 3:14-19; Mat. 6:25-27, 31-33)

© 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania

CA-brpgm26-CN