Pulogalamu ya Msonkhano wa 2026 Wakuti Chimwemwe Chosatha
Lachisanu
Pulogalamu ya Lachisanu yachokera pa Mateyu 5:3—“Osangalala ndi anthu amene amazindikira zosowa zawo zauzimu.”
Loweruka
Pulogalamu ya Loweruka yachokera pa Machitidwe 20:35—“Kupatsa kumatichititsa kukhala osangalala kwambiri kuposa kulandira.”
Lamlungu
Pulogalamu ya Lamlungu yachokera pa Mateyu 13:16—“Ndinu osangalala chifukwa maso anu amaona komanso makutu anu amamva.”
Mawu kwa Osonkhana
Mawu othandiza anthu amene asonkhana.
Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi
ZOKHUDZA IFEYO
Dzabwereni ku Msonkhano wa 2026—“Chimwemwe Chosatha”
Tikukuitanirani ku Msonkhano wa masiku atatu wachaka chino wa Mboni za Yehova.
MISONKHANO IKULUIKULU
Mukuitanidwa Kumsonkhano wa Mboni za Yehova wa 2026 Wakuti “Chimwemwe Chosatha”
Bwerani kuti mudzakhale nafe Pamsonkhano wa 2026 wakuti “Chimwemwe Chosatha” kuti mudzaphunzire mmene kukhala pa ubwenzi wabwino ndi Mlengi, kungakuthandizireni kupeza chimwemwe chosatha.
MISONKHANO IKULUIKULU
Zimene Zili Muvidiyo Yakuti: Uthenga Wabwino wa Yesu, Gawo 4, 5 ndi 6
N’chifukwa chiyani anthu ankabwera kwa Yesu? Nanga zimene ankalankhula zitasiyana ndi zimene atsogoleri achipembedzo ankakhulupirira, chinachitika n’chiyani?

