POTENGERA DERA

Azerbaijan

Chichewa
Azerbaijan
/assets/ct/28ada02fb0/images/syn_placeholder_sqr.png

Azerbaijan

 

2015-08-12

AZERBAIJAN

A Mboni za Yehova Akufunitsitsa Kuti Boma la Azerbaijan Litulutse Azimayi Awiri Amene Anamangidwa Popanda Mlandu

Mayi Irina Zakharchenko ndi mayi Valida Jabrayilova akuchitidwa zinthu ngati zigawenga zoopsa chifukwa chouza ena zimene amakhulupirira. Kodi boma la Azerbaijan liyamba kutsatira malamulo ake olemekeza ufulu wachipembedzo?

2015-12-07

AZERBAIJAN

Dziko la Azerbaijan Likupitirizabe Kuphwanya Ufulu Wachipembedzo

Akuluakulu a boma akusokoneza misonkhano ya Mboni za Yehova yomwe amaichita mwamtendere ndipo akuwalipiritsa ndalama zambiri komanso a Mboni ena akumangidwa. Kodi akuluakulu a boma la Azerbaijan athandiza kuti zinthu ziyambe kuyenda mwachilungamo?

2014-05-29

AZERBAIJAN

A Mboni za Yehova ku Azerbaijan Adandaula ku Khoti Loona za Ufulu wa Anthu ku Ulaya

Boma la Azerbaijan limati limapereka chitsanzo chabwino pa nkhani yolemekeza ufulu wolambira. Koma n’zodabwitsa kuti bomali limapondereza anthu a Mboni za Yehova.