Mfundo Zachidule—Reunion
- 896,000—Chiwerengero cha anthu
- 3,639—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
- 41—Mipingo
- Pa anthu 251 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

Ku Plage de Boucan Canot, ku Réunion—Makolo a Mboni akuwerenga buku lakuti Zimene Tingaphunzire Munkhani za m’Baibulo limodzi ndi mwana wawo wamwamuna
M’tawuni ya Saint-Leu ku Réunion—Wa Mboni akuonetsa vidiyo yakuti Kodi pa Nyumba ya Ufumu Pamachitika Zotani? m’Chikiriyoli cha ku Réunion